FATHERS LOVE LETTER .COM
  • Home
  • About
    • About
    • Contact
    • Copyright
    • Donate
    • FAQ
    • Our Vision
    • Our Websites
    • Privacy Policy
    • Terms of use
    • The Story
    • What We Believe
  • Media Formats
    • Media Center
    • HD Video
    • 25th Anniversary Video
    • Vertical Video
    • Video History
    • Stores
    • Text
    • Audio
    • Kids FLL
  • Languages
  • God and You
  • FLL Book
    • Devotional Index
    • Free Audiobook
    • Free eBook

Nyanja
Father's Love Letter

The Nyanja Father's Love Letter is currently available
in the following formats...
1. An instrumental video version
2. An online text version
Please feel free to copy this text and design your own version
of the Nyanja Father's Love Letter.
Nyanja is a language used by many in countries which border the Zambezi, in Africa. Nyanja is a language spoken in Malawi, many parts of Zambia, Mozambique and other areas.

Nyanja Father's Love Letter Instrumental Video

Video Courtesy of Berge Boyadjian

Nyanja Father's Love Letter


KALATA WACIKONDI CA ATATE
Kulila kwa Mtima wa Atate kucokera ku Genesis kufikira ku Cibvumbulutso.

Mwana wanga

Siungandidziwe Ine,
koma Ine ndidziwa zones za iwe
Masalmo 139:1

Ndidziwa kukhala kwako ndi kuuka kwako
Masalmo 139:2

Ndizolowera nazo njira zako zonse
Masalmo 139:3

Komatu matsitsi onse a m'mutu mwako awerengedwa
Mateyu 10:29-31

Pakuti iwe unalengedwa m'cifanizo canga
Genesis 1:27

Mwa ine ukhala ndi kuyendayenda
ndi kupeza mkhalidwe wako
Macitidwe a Atumwi 17:28

Pakuti iwe ndiwe mbadwo wanga
Macitidwe a Atumwi 17:28

Ndinakudziwa iwe usanalengedwe M'mimba
Yeremiya1:4-5

Ndinakusankha pomwe ndinakonzekeratu cilengedwe
Aefeso 1:11-12

Sunakhalako molakwitsa
Masalmo 139:15-16

Masiku ako onse ndiolembedwa m'buku langa
Masalmo139:15,16

Ndinapangiratu nyengo ya
kubadwa kwako ndi pokhala pako
Macitidwe a Atumwi 17:26

Unapangidwa moopsa ndi modabwisa
Masalmo 139:14

Ndinakuumba M'mimba mwa a mako
Masalmo 139:13

Ndikukutulutsa pa tsiku lobadwa iwe
Masalmo 71:6

Anandionetsera monama iwo amene sandidziwa
Yohane 8:41-44

Sindiri kutali ndiponso wamkwiyo,
koma ndine coonetsera canthunthu ca cikondi
1 Yohane 4:16

Ndifunitsitsa kuonetsera cikondi canga pa iwe
1 Yohane 3:1

Cifukwa cakuti ndiwe mwana
wanga ndipo Ine ndine Atate wako
1 Yohane 3:1

Ndipatsa kwa iwe mopambana,
kuposa atate wako - wapadziko lapansi
Mateyu 7:11

Pakuti ndine Atate wangwiro
Mateyu 5:48

Mphatso iri yonse yabwino imene
ulandira icokera mdzanja langa
Yakobo 1:17

Pakuti Ndine amene ndikupatsa
ndi kukwaniritsa zofuna zako zonse
Mateyu 6:31-33

Makonzedwe anga atsogolo lako
akhala ozara ndi ciyembekezo
Yeremiya 29:11

Cifukwa ndikukonda ndi cikondi camuyaya
Yeremiya 31:3

Malingaliro anga paiwe ndi oculuka koposa mcenga
Masalmo 139:17,18

Ndisekerera nawe ndi kuyimbirapo
Zefaniya 3:17

Sindidzaleka kukucitira zabwino
Yeremiya 32:40

Cifukwa ndiwe Cuma canga ca padera
Eksodo 19:5

Ndifuna kukuoka ndi mtima wanga
wonse ndi moyo wanga wonse
Yeremiya 32:41

Ndipo ndifuna kukuonetsa iwe zazikuru ndi zolakika
Yeremiya 33:3

Ngati undifunafuna ndi mtima wako wonse,
udzandipeza
Deuteronomo 4:29

Udzikondweretsenso mwa Ine ndipo
ndidzakupatsa zokhumba mtima wako
Masalmo 37:4

Pakuti wakupatsa zokhumbazo ndine
Afilipi 2:13

Ndingathe kucita koposatu zimene uziganizira
Aefeso 3:20

Pakuti ndine wakukulimbikitsa wam'kuru
2 Atesalonika 2:16-17

Ndinenso Atate wako wakukutonthoza
iwe m'masautso ako onse
2 Akorinto1:3-4

Pamene mtimo wako ndi wosweka ndili pafupi ndi iwe
Masalmo 34:18

Monga momwe Mbusa atengera nkhosa,
ndakutengo iwe pacifuwa canga
Yesaya 40:11

Tsiku limodzi ndidzakupukutira misozi
yonse kuicotsa pamaso pako
Cibvumbulutso 21:3-4

Ndipo ndidzasotsa cowawitsa conse
cimene unakhala naco padziko lapansi
Cibvumbulutso 21:3-4

Ine ndine Atate wako, ndipo ndikukonda
monga momwe ndikonda mwana wanga, Yesu
Yohane 17:23

Pakuti mwa Yesu, cikondi canga pa iwe cinaonetsedwa
Yohane 17:26

Iye ali cizindikilo ceni ceni ca cikhalidwe canga
Ahebri 1:3

Anadza kuonetsera kuti sinditsutsana nawe,
koma ndili wako
Aroma 8:31

Ndikukuudza kuti sindiwerengera macimo ako
2 Akorinto 5:18-19

Yesu anafa kotero kuti iwe ndi
Ine tikhale m'ciyanjano
2 Akorinto 5:18-19

Imfa yace inakhala cionetsero
cacikondi canga pa iwe
1 Yohane 4:10

Ndinapereka zokondedwa zanga zonse
kuti ndipeze cikondi cako
Aroma 8:31-32

Ngati ulandira mphaso ya mwana wanga, Yesu,
ulandira Ine
1 Yohane 2:23

Ndipo kulibe kanthu kalikonse kamene
kadzakusiyanitsa kucikondi canga
Aroma 8:38-39

Bwera kuli Ine ndipo ndidzapanga phwando
yaikuru imene ngakhale m'mwamba siinakhalako
Luka 15:7

Matsiku onse ndinakhala Atate ndipo ndidzakhalabe Atate
Aefeso 3:14-15

Funso langa ndi ili ….
Kodi udzakhala mwana wanga?
Yohane 1:12-13

Ndiyembekezera iwe…
Luka 15:11-32


Cikondi, Atate Wako
Wamphamvu zonse


ACKNOWLEDGEMENTS / PERMISSION:
Please feel free to copy and share all of the resources on this page as long as you do so free of charge.

About Us

About
The Story
Copyright

Get Involved

FAQ
Terms of Use
Our Websites

Connect

Contact
Privacy Policy
Donate
© COPYRIGHT 2025. ALL RIGHTS RESERVED.
  • Home
  • About
    • About
    • Contact
    • Copyright
    • Donate
    • FAQ
    • Our Vision
    • Our Websites
    • Privacy Policy
    • Terms of use
    • The Story
    • What We Believe
  • Media Formats
    • Media Center
    • HD Video
    • 25th Anniversary Video
    • Vertical Video
    • Video History
    • Stores
    • Text
    • Audio
    • Kids FLL
  • Languages
  • God and You
  • FLL Book
    • Devotional Index
    • Free Audiobook
    • Free eBook